Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 317-318 Nsanja ya Olonda,4/1/2000, tsa. 148/15/1994, tsa. 31
16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+