Deuteronomo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzachititsa adani anu amene adzakuukireni kugonja pamaso panu.+ Pobwera kudzakuukirani adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso panu, adzadutsa njira zosiyanasiyana 7.+ Salimo 68:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Mulungu anyamuke, adani ake amwazike,Ndipo amene amadana naye athawe pamaso pake.+
7 Yehova adzachititsa adani anu amene adzakuukireni kugonja pamaso panu.+ Pobwera kudzakuukirani adzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso panu, adzadutsa njira zosiyanasiyana 7.+