-
Yesaya 30:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Kuwala kwa mwezi wathunthu kudzakhala ngati kuwala kwa dzuwa. Ndipo kuwala kwa dzuwa kudzakhala kwamphamvu kwambiri kuwonjezeka maulendo 7,+ ngati kuwala kwa masiku 7. Zimenezi zidzachitika pa tsiku limene Yehova adzamange mabala* a anthu ake+ amene anavulala ndi kuchiritsa mabala aakulu amene anavulala pamene ankawalanga.+
-