13 Ndikomereni mtima inu Yehova. Inu amene mukundichotsa pakhomo la imfa,+
Onani mmene anthu amene akudana nane akundizunzira,
14 Kuti ndilengeze ntchito zanu zotamandika pamageti a mwana wamkazi wa Ziyoni,+
Komanso kuti ndisangalale chifukwa mwandipulumutsa.+