11 Chifukwa onse, woyeretsa ndi amene ayeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Choncho iye sachita manyazi kuwatchula kuti “abale” ake,+ 12 pamene akunena kuti: “Ndidzalengeza dzina lanu kwa abale anga. Ndidzakutamandani poimba nyimbo pakati pa mpingo.”+