Ekisodo 19:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe komanso mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa Aisiraeli.” Yesaya 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+Iwe Yakobo, amene ndakusankha,+Mbadwa* ya mnzanga Abulahamu.+
5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe komanso mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa Aisiraeli.”
8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+Iwe Yakobo, amene ndakusankha,+Mbadwa* ya mnzanga Abulahamu.+