35 Aisiraeli anachita zimene Mose anawauza ndipo anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide komanso zovala.+ 36 Choncho Yehova anachititsa kuti Aiguputo akomere mtima anthu ake, moti Aiguputowo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+