Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Chifukwa wachita zinthu zodabwitsa.+ Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.*+ Salimo 139:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndimakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa+ ndipo zimenezi zimandichititsa mantha. Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ine ndikudziwa bwino zimenezi. Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
98 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Chifukwa wachita zinthu zodabwitsa.+ Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.*+
14 Ndimakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa+ ndipo zimenezi zimandichititsa mantha. Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ine ndikudziwa bwino zimenezi.
3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+