Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+ Salimo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nʼzosilirika kuposa golide,Kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+Ndipo nʼzotsekemera kuposa uchi,+ kuposa uchi umene ukukha mʼzisa. Salimo 119:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Chilamulo chimene mwapereka nʼchabwino kwa ine,+Nʼchabwino kwambiri kuposa ndalama zagolide ndi zasiliva masauzande ambiri.+
8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+
10 Nʼzosilirika kuposa golide,Kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+Ndipo nʼzotsekemera kuposa uchi,+ kuposa uchi umene ukukha mʼzisa.
72 Chilamulo chimene mwapereka nʼchabwino kwa ine,+Nʼchabwino kwambiri kuposa ndalama zagolide ndi zasiliva masauzande ambiri.+