Yesaya 48:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+ Yohane 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinalembedwa mʼMabuku a Aneneri kuti: ‘Onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine. Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+
17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+
45 Zinalembedwa mʼMabuku a Aneneri kuti: ‘Onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru, azipempha kwa Mulungu+ ndipo adzamupatsa,+ chifukwa iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.*+