11 Iwo anayamba kuimba+ potamanda ndi kuyamika Yehova kuti, “iye ndi wabwino, chikondi chokhulupirika chimene amachisonyeza kwa Isiraeli chidzakhalapo mpaka kalekale.”+ Kenako anthu onse anafuula kwambiri potamanda Yehova chifukwa cha kumangidwa kwa maziko a nyumba ya Yehova.