Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyera.+Ali ngati siliva woyengedwa mungʼanjo yadothi nthawi zokwanira 7. Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+
8 Malamulo ochokera kwa Yehova ndi olungama, amasangalatsa mtima.+Chilamulo cha Yehova ndi choyera, chimatsegula maso.+