15 Kenako Mulungu anauzanso Mose kuti:
“Aisiraeli ukawauze kuti, ‘Yehova Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo,+ wandituma kwa inu.’ Dzina langa ndi limeneli mpaka kalekale,+ ndipo mibadwo yonse izidzakumbukira dzina limeneli.