15 Kenako Mulungu anauzanso Mose kuti:
“Zimene ukauze ana a Isiraeli ndi izi, ‘Yehova Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abulahamu,+ Mulungu wa Isaki+ ndi Mulungu wa Yakobo,+ wandituma kwa inu.’ Limeneli ndilo dzina langa mpaka kalekale,+ ndipo ndicho chondikumbukirira ku mibadwomibadwo.+