2 Samueli 22:50, 51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Nʼchifukwa chake ndidzakuyamikani inu Yehova pakati pa mitundu ya anthu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ 51 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake;+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”+ 1 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muimbireni, muimbireni nyimbo* zomutamanda,+Ganizirani mozama* ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso kuti anthu a mitundu ina alemekeze Mulungu chifukwa cha chifundo chake,+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+
50 Nʼchifukwa chake ndidzakuyamikani inu Yehova pakati pa mitundu ya anthu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ 51 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake;+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.”+
9 Komanso kuti anthu a mitundu ina alemekeze Mulungu chifukwa cha chifundo chake,+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+