Numeri 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova akuyangʼaneni mokondwera ndipo akupatseni mtendere.”’+ Salimo 80:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, tibwezeretseni mwakale.Walitsani nkhope yanu pa ife kuti tipulumutsidwe.+ Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+
7 Inu Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, tibwezeretseni mwakale.Walitsani nkhope yanu pa ife kuti tipulumutsidwe.+
15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+
12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+