Salimo 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+ Zimenezi zinditsogolere.+Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+ Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+ Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+
3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+ Zimenezi zinditsogolere.+Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+
11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+ Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+ Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+