Miyambo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amayangʼanira pakamwa pake* amateteza moyo wake,+Koma amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+ Miyambo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakamwa pa munthu wopusa mʼpamene pamamuchititsa kuti awonongedwe,+Ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.
3 Amene amayangʼanira pakamwa pake* amateteza moyo wake,+Koma amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+
7 Pakamwa pa munthu wopusa mʼpamene pamamuchititsa kuti awonongedwe,+Ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.