Yesaya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje+Ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a mʼnyanja.+
18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje+Ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a mʼnyanja.+