Miyambo 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu wosaugwira mtima+Ali ngati mzinda umene mpanda wake wagumulidwa. Miyambo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wopusa amatulutsa mkwiyo wake wonse,+Koma wanzeru amakhala wodekha ndipo amalamulira mkwiyo wake.+ Mlaliki 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usamafulumire kukwiya,+ chifukwa anthu opusa ndi amene sachedwa kukwiya.*+
11 Munthu wopusa amatulutsa mkwiyo wake wonse,+Koma wanzeru amakhala wodekha ndipo amalamulira mkwiyo wake.+