5 Inu amene mumanena kuti: ‘Kodi chikondwerero cha nthawi imene mwezi watsopano waoneka chitha liti+ kuti tiyambe kugulitsa mbewu zathu?
Sabata+ litha liti kuti tiyambe kutsatsa mbewu zathu,
Kuti tichepetse muyezo wa efa,
Tiwonjezere kulemera kwa sekeli,
Komanso kuti tibere anthu ndi masikelo athu achinyengo?+