Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwe wokongola kwambiri pakati pa ana a anthu. Mʼkamwa mwako mumatuluka mawu osangalatsa.+ Nʼchifukwa chake Mulungu wakudalitsa mpaka kalekale.+ Miyambo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mawu achilungamo amasangalatsa mafumu. Iwo amakonda munthu amene amalankhula moona mtima.+ Mateyu 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Osangalala ndi anthu oyera mtima+ chifukwa adzaona Mulungu.
2 Ndiwe wokongola kwambiri pakati pa ana a anthu. Mʼkamwa mwako mumatuluka mawu osangalatsa.+ Nʼchifukwa chake Mulungu wakudalitsa mpaka kalekale.+