Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:2 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 48/15/2002, tsa. 123/1/1987, tsa. 23
2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+