Salimo 119:115 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 115 Mukhale kutali ndi ine, anthu oipa inu,+Kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga. Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu,+Ndipo ndimanyansidwa ndi anthu amene amakupandukirani.+
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu,+Ndipo ndimanyansidwa ndi anthu amene amakupandukirani.+