21 Iwo adzamanga nyumba nʼkumakhalamo,+
Ndipo adzadzala minda ya mpesa nʼkudya zipatso zake.+
22 Sadzamanga nyumba kuti wina azikhalamo,
Kapena kudzala kuti ena adye.
Chifukwa masiku a anthu anga adzakhala ngati masiku a mtengo,+
Ndipo anthu anga osankhidwa adzasangalala mokwanira ndi ntchito ya manja awo.