Mlaliki 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo ndinapitiriza kuchitabe zinthu mwanzeru.
9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo ndinapitiriza kuchitabe zinthu mwanzeru.