Salimo 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uzikhulupirira Yehova ndipo uzichita zabwino.+Ukhale padziko lapansi* ndipo uzichita zinthu mokhulupirika.+ 1 Atesalonika 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onetsetsani kuti pasapezeke wobwezera choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse muziyesetsa kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+
3 Uzikhulupirira Yehova ndipo uzichita zabwino.+Ukhale padziko lapansi* ndipo uzichita zinthu mokhulupirika.+
15 Onetsetsani kuti pasapezeke wobwezera choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse muziyesetsa kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+