Yesaya 60:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 “Imirira mkazi iwe!+ Onetsa kuwala kwako, chifukwa kuwala kwako kwafika. Ulemerero wa Yehova wakuunikira.+ Yesaya 60:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzuwa lako silidzalowanso,Ndipo mwezi wako sudzasiya kuwala,Chifukwa Yehova adzakhala kuwala kwako mpaka kalekale,+Ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+
60 “Imirira mkazi iwe!+ Onetsa kuwala kwako, chifukwa kuwala kwako kwafika. Ulemerero wa Yehova wakuunikira.+
20 Dzuwa lako silidzalowanso,Ndipo mwezi wako sudzasiya kuwala,Chifukwa Yehova adzakhala kuwala kwako mpaka kalekale,+Ndipo masiku ako olira adzakhala atatha.+