Yesaya 41:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Anthu ovutika ndi osauka akufunafuna madzi, koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma chifukwa cha ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+ Yeremiya 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo adzabwera akulira.+ Ndidzawatsogolera akadzandipempha kuti ndiwakomere mtima. Ndidzawatsogolera kumitsinje ya madzi,*+Ndipo ndidzawayendetsa mʼnjira yabwino imene sadzapunthwa. Chifukwa ine ndine Bambo ake a Isiraeli ndipo Efuraimu ndi mwana wanga woyamba kubadwa.”+
17 “Anthu ovutika ndi osauka akufunafuna madzi, koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma chifukwa cha ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+
9 Iwo adzabwera akulira.+ Ndidzawatsogolera akadzandipempha kuti ndiwakomere mtima. Ndidzawatsogolera kumitsinje ya madzi,*+Ndipo ndidzawayendetsa mʼnjira yabwino imene sadzapunthwa. Chifukwa ine ndine Bambo ake a Isiraeli ndipo Efuraimu ndi mwana wanga woyamba kubadwa.”+