-
Deuteronomo 15:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Samalani kuti musakhale ndi maganizo oipa awa mumtima mwanu akuti, ‘Chaka cha 7 choti anthu angongole amasuke chayandikira,’+ nʼkulephera kuthandiza mʼbale wanu wosaukayo mowolowa manja, osamupatsa chilichonse. Ngati atafuulira Yehova chifukwa cha zimene inuyo mwamuchitira, mudzakhala kuti mwachimwa.+
-