20 “Kodi Efuraimu si mwana wanga wamtengo wapatali, amene ndimamukonda?+
Ngakhale kuti nthawi zambiri ndimamudzudzula, ndimamukonda ndipo ndimamukumbukirabe.
Nʼchifukwa chake ndakhudzika naye kwambiri.+
Ndipo sindidzalephera kumumvera chisoni,” akutero Yehova.+