Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake+Akadzaona kuti mphamvu zawo zatha,Komanso kuti kwangotsala anthu ovutika ndi ofooka. Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamvera chisoni atumiki ake+Akadzaona kuti mphamvu zawo zatha,Komanso kuti kwangotsala anthu ovutika ndi ofooka.
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+