Yesaya 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli. Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+
14 “Usachite mantha, nyongolotsi* iwe Yakobo,+Inu amuna a mu Isiraeli, ineyo ndikuthandizani,” akutero Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli.
20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+