Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’
10 Usachite mantha, chifukwa ndili ndi iwe.+ Usade nkhawa chifukwa ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa, ndithu ndikuthandiza,+Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja lachilungamo.’