-
Hoseya 1:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndipo Aisiraeli* adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene ankauzidwa kuti, ‘Siinu anthu anga,’+ adzauzidwa kuti, ‘Ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+ 11 Ayuda ndi Aisiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzasankha mtsogoleri mmodzi nʼkutuluka mʼdzikolo chifukwa tsiku limeneli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.”+
-