-
Amosi 9:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ‘Pa tsiku limenelo, ndidzadzutsa nyumba* ya Davide+ imene inagwa,
Ndi kukonza malo amene khoma lake linawonongeka.
Ndidzaikonza kuti isakhalenso bwinja.
Ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati mmene inalili kale.+
12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga atenge zinthu zotsala za Edomu.+
Ndiponso za mitundu yonse ya anthu imene inkaitanira pa dzina langa,’ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.
-