Deuteronomo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni. Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+ Deuteronomo 28:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chakuti simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu.
27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni.
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chakuti simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu.