2 Mafumu 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako mfumu ya Asuri inatenga anthu kuchokera ku Babulo, ku Kuta, ku Ava, ku Hamati ndi ku Sefaravaimu+ nʼkuwaika mʼmizinda ya ku Samariya mʼmalo mwa Aisiraeli. Anthuwo anatenga Samariya nʼkumakhala mʼmizinda yake. Yesaya 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi milungu ya Hamati ndi Aripadi+ ili kuti? Nanga milungu ya Sefaravaimu+ ili kuti? Kodi yapulumutsa Samariya mʼmanja mwanga?+
24 Kenako mfumu ya Asuri inatenga anthu kuchokera ku Babulo, ku Kuta, ku Ava, ku Hamati ndi ku Sefaravaimu+ nʼkuwaika mʼmizinda ya ku Samariya mʼmalo mwa Aisiraeli. Anthuwo anatenga Samariya nʼkumakhala mʼmizinda yake.
19 Kodi milungu ya Hamati ndi Aripadi+ ili kuti? Nanga milungu ya Sefaravaimu+ ili kuti? Kodi yapulumutsa Samariya mʼmanja mwanga?+