Ezekieli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndidzamuponyera ukonde wanga ndipo iye adzakodwa mu ukonde wanga wosakira.+ Kenako ndidzamupititsa ku Babulo, kudziko la Akasidi. Koma iye sadzaliona dzikolo ndipo adzafera komweko.+
13 Ine ndidzamuponyera ukonde wanga ndipo iye adzakodwa mu ukonde wanga wosakira.+ Kenako ndidzamupititsa ku Babulo, kudziko la Akasidi. Koma iye sadzaliona dzikolo ndipo adzafera komweko.+