Yesaya 63:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+ Kenako iye anakhala mdani wawo,+Ndipo anachita nawo nkhondo.+ Ezekieli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anapitiriza kundiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa Aisiraeli,+ ku mitundu ya anthu amene andipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+
10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+ Kenako iye anakhala mdani wawo,+Ndipo anachita nawo nkhondo.+
3 Iye anapitiriza kundiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa Aisiraeli,+ ku mitundu ya anthu amene andipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+