22 Komanso anapanga zozimitsira nyale, mbale zolowa, makapu ndi zopalira moto. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino. Anapanganso khomo lolowera mʼnyumbayo, zitseko zamkati za Chipinda Choyera Koposa+ ndi zitseko za nyumbayo. Zonsezi zinali zagolide.+