Yesaya 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka.Phokoso la anthu amene akusangalala latha.Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze sizikumvekanso.+ Yeremiya 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala mʼmalowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.
8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka.Phokoso la anthu amene akusangalala latha.Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze sizikumvekanso.+
10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala mʼmalowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.