Yeremiya 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi,+ mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu, chifukwa dzikoli lidzawonongedwa nʼkukhala mabwinja okhaokha.’”+
34 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi,+ mʼmizinda ya Yuda ndi mʼmisewu ya Yerusalemu, chifukwa dzikoli lidzawonongedwa nʼkukhala mabwinja okhaokha.’”+