Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+ 2 Samueli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nʼchifukwa chake ndinudi wodabwitsa,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Palibe amene angafanane ndi inu+ komanso palibe Mulungu wina koma inu nokha.+ Zonse zimene tamva zikutsimikizira zimenezi. Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+
11 Ndi mulungu uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+ Mumasonyeza kuti ndinu woyera koposa,+ ndani angafanane ndi inu? Ndinu woyenera kuopedwa ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda. Inu mumachita zodabwitsa.+
22 Nʼchifukwa chake ndinudi wodabwitsa,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Palibe amene angafanane ndi inu+ komanso palibe Mulungu wina koma inu nokha.+ Zonse zimene tamva zikutsimikizira zimenezi.
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+