Yesaya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema,Amene akuuza zifaniziro zachitsulo* kuti: “Ndinu milungu yathu,”+Adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri. Yesaya 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anzake onse adzachititsidwa manyazi,+ Amisiriwo ndi anthu basi. Onsewo asonkhane pamodzi ndipo akhale pamalo awo. Adzachita mantha ndipo onsewo adzachititsidwa manyazi.
17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema,Amene akuuza zifaniziro zachitsulo* kuti: “Ndinu milungu yathu,”+Adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.
11 Anzake onse adzachititsidwa manyazi,+ Amisiriwo ndi anthu basi. Onsewo asonkhane pamodzi ndipo akhale pamalo awo. Adzachita mantha ndipo onsewo adzachititsidwa manyazi.