Yeremiya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abulu amʼtchire angoima mʼmapiri opanda kanthu. Akupuma mwawefuwefu ngati mimbulu.Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+ Yeremiya 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzikoli ladzaza ndi anthu achigololo.+Chifukwa cha matemberero, dziko likulira maliro+Ndipo malo amʼchipululu odyetserako ziweto auma.+ Zochita za anthuwa ndi zoipa ndipo akugwiritsa ntchito mphamvu zawo molakwika.
6 Abulu amʼtchire angoima mʼmapiri opanda kanthu. Akupuma mwawefuwefu ngati mimbulu.Maso awo achita mdima chifukwa kulibe msipu.+
10 Dzikoli ladzaza ndi anthu achigololo.+Chifukwa cha matemberero, dziko likulira maliro+Ndipo malo amʼchipululu odyetserako ziweto auma.+ Zochita za anthuwa ndi zoipa ndipo akugwiritsa ntchito mphamvu zawo molakwika.