-
Yoweli 1:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ngakhale ziweto zikubuula.
Magulu a ngʼombe akuyendayenda mosokonezeka chifukwa palibe msipu.
Ndiponso magulu a nkhosa alangidwa.
-