-
Deuteronomo 4:27, 28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Yehova adzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo anthu ochepa okha pakati panu ndi amene adzapulumuke+ mʼmayiko a mitundu imene Yehova adzakuthamangitsireni. 28 Kumeneko mudzatumikira milungu yamtengo ndi mwala, yopangidwa ndi manja a anthu,+ milungu imene singaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.
-