-
Ezekieli 20:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Inu a nyumba ya Isiraeli, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Pitani, aliyense wa inu akatumikire mafano ake onyansa.+ Koma mudziwe kuti ngati simuyamba kundimvera, nthawi idzafika ndipo simudzathanso kudetsa dzina langa loyera popereka nsembe zanu ndiponso polambira mafano anu onyansa.’+
-