Yeremiya 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu awa uwauze kuti,‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi masana ndipo asasiye,+Chifukwa mwana wamkazi wa anthu anga, yemwe ndi namwali, waphwanyidwa kotheratu+Ndipo ali ndi bala lalikulu kwambiri. Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulira chifukwa cha zinthu zimenezi.+ Misozi ikutuluka mʼmaso mwanga. Chifukwa aliyense amene akananditonthoza kapena kunditsitsimula, ali kutali ndi ine. Ana anga awonongedwa ndipo mdani wanga wapambana.
17 Anthu awa uwauze kuti,‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi masana ndipo asasiye,+Chifukwa mwana wamkazi wa anthu anga, yemwe ndi namwali, waphwanyidwa kotheratu+Ndipo ali ndi bala lalikulu kwambiri.
16 Ndikulira chifukwa cha zinthu zimenezi.+ Misozi ikutuluka mʼmaso mwanga. Chifukwa aliyense amene akananditonthoza kapena kunditsitsimula, ali kutali ndi ine. Ana anga awonongedwa ndipo mdani wanga wapambana.